ZIONE PART ONE(1)
Analibe ntengo ogwira tsikanayo ndiye anakatani iye adapakulisa kuti apeze chokudya ndipogona..
kalionela avulalitsa zione sikanayu anali okongola zed ndipo amachoka pankomo pakwawo osadya pena ndiye chimakhala chithu chomwe amawauza amzake pafupi pa fupi..
njala ikundiwawa poti sindinadye bambo anga anapuma ntchito ndipo akudila ndalama za peshoni ndiye kupeza ndalama kukumakhala kowavuta..
aaaaaaaaa iwe tsikana wabwino bwino ngati iwe chochita chikukusowa aaaaa koma aa gerl muli serious? tangoona ma phone omwe tikuyuza simanyakatu inu munakaphabe sikizi tobwa tobwa inu a girl mulibe look sharp
Anatelo wangi pomukopa zioneyo ndipo zione adafusa look sharp nde chani a girl ndithandizeni ine nzanu....
mmmmm inu a girl ndikamodzi kokhatu mfwenfwe kuno ndipo a girl simungakhale manyaka
zione ntima pha pha pha akaganizira uphawi.omwe uli kwawo ndipo linali loweruka anamutenga zione kukayenda nawe...
Ndipo ali kuyenda wangi phone inaitana pakuyankha kwake anvekele mmm inu mpaka pul
Comments