ZIONE PART 3
ZIONE ππ
Zione atamaliza kugonana ndi blessor yo anali paulendo obwelera kwao ndipo ali mu njira anakumana ndi abusa ndipo abusa atamuona zione anali osowa ntendere ndipo anafusa.zione kodi uli bwino bwino
zione ayankha eya ndili bwino bwanji nduoneka ngati odwala dwala kapena wanjala .....
abusa ayi si choncho kungoti ndinali ndi maloto ako dzulo koma anali onvesa chisoni moyo wako unaonongeka ngati wachinyama
abusa anapitiliza ndinakakonda unakabwera kunyumba tizakhare ndimapemphero monga kare ndipo zione anawa yankha motere...
moti anthu inu simumanva bwino pamene wina akusangalala eti basi inuyo kukula chimutu choncho nkumalota zaine maloto anatha et kapena munangokula mwa uchisiru choncho munali kuti pomwe ndimavutika ...
mmmmm bwanji simunabwere ndimaloto ndili billioneya dzithe zopusa ine ayi anatha mau zione kwa abusawo.ndipo azione apepesedwa ...
atafika kwawo makolo ake anali akumudikiraso kuti amulangize afika.zione ndipo makolo ake ayambapo
zione mwana wanthu t

Comments