JOYCE
Aulowa umasiye Joyce kamba ka usilu wake mayi ake amwalira kamba kazilakolako zake apa bambo ake ndi anthu Ena anapanga madongosolo amaliro
Kenako bambo a Joyce apeza mwayi omasuka sinakha apa sangamazembereso koma azingogonana ndi mwana wawoyi momamasuka
Ndipo Joyce anali mugulu lokafuna thandizo poti mimba yakeyi inakwana miyezi 13 asanachirebe ndipo anthu anayamba kunena zambiri poti mbiri sigonera anachitawo ndi malaulo ndi mwikho mmm mwana opanda matha
Anthu Ena azikhulupiliro anayamba kumuuza kuti zimu wa mayi ake ndi omwe akumupangisa zimenezo zimu wawo udakali okwiya ndipo muzisamba anauzidwa kuti sakhalisa amwalira
JOYCE
Ukapanga chipongwe munthu supanga zolongosoka ndipo patadusa ma tsiku ochepa bambo a Joyce anapenga misala ndipo amazilumaluma okha okha ndipo anthu sanadabweso poti anaziwa kuti masoka akuwasata zimu wankaz wake ukumuzuza
Atayima mutu joyce mayi ake atafa chifukwa chaiye ndi bambo ake ndipo bambo ake atapenga misala koma so iyeyo mimba yomwe anagona ndi bambo akeyo mpaka miyezi 19
Apa anaganiza zongokapanga za opaleshoni kuti apeze ntendere poti anali kusausika ndi ululu tsiku ndi tsiku
Ndipo ma siku akuchipata kuti akapangidwe opaleshoni atafika ndipo iye sanamulore kuti afe koma so kuti mwana wake afe koma anve kuwawa
Joyce anapangidwa opaleshoni koma pomwe ankamutulusa mwana a anali be mwendo umodzi ndipo mwana yo anali wankaz anali wakhulu choncho poti anabadwa mwezi wa 20
JOYCE anatulusidwa kuchipatala ndipo atafika kwawo anabisa mwana wake kuti anthu Asamuone poti alibe mwendo umodzi ndipo apo anayamba kuboweka nawe mwana yo ndipo anayamba kuganiza kuti ndivuto loonjezera poti anthu azimuseka ndikumutoza
Joyce mabala ONSE ankangophulika ndipo kumangonyeka moti madokotala anamuuza kuti sangakwaniseso kusoka ndipo mwana uja anali ovuta akayamba kulira zinali ngat akukumba mabala ndipo amaboweka nawe kambiri
Patadusa ma week awiri Joyce atatopa ndiululu koma so kutozedwa anaganiza zongozipha kuti akapume koma mmm vula ikakuona lisiro sikata Joyce anatenga chingwe ndipo atazinyonga anthu anamupulumusa kotero anamupitisa kupolisi ndipo apolisi atamuona Joyce nyengo yomwe Ali anangomutulusa
Ndipo apo Joyce alibe ntendere ndipo alibe mwayi or pang'ono
Osama panga chipongwe anthu omwe amatikonda koma so omwe timawakonda osamayiwala makolo Ali ngat Mulungu wanthu wachiwiripa Ali kalikiliki kupephela kuti Achille
Comments