PATUMA KUSANVA
Ali ndi dzana 6 mama changu ndichedwatu kusukulu ok mwana wanga koma kodi umafuna uzakhale ndani ukazamaliza sukulu,,,,
ndimafuna ndizakhale dokotala ok mwana wanga patuma anali ndi mayi abwino omwe amamulangiza tsiku ndi siku kuchokera ali mwana zokhuza makhalidwe abwino ,,,,
patuma anathesa ndikuyamba chibwez ndi aphuzisi ake moti mpaka anagonana kangapo konse
nkhani inavuta nkazi wamphuzisiyi atayinva anakwiya zed ndipo anapita kusukulu konko namugwila patuma
anamumenya mpaka thapsa anamuvula zovala zonse ndi pant yemwe.kuti aone chomwe akusatira.amunake.
Comments